Anagkazo Mphamvu Yokakamiza!

Anagkazo amatanthauza “kukakamiza”.Amatanthauzanso kupangitsa kuti chifunike, kukusira, ndi kupanikiza mwa njira iliyonse monga kuumiriza, kuwopseza, kukopa ndi kuchonderera. Nthawi zina tiyenera kubwerera ku Chigiriki kuti timvetsetse matanthauzo enieni la mawu ena a M’baibulo. Mukuona, Chipangano Chatsopano chinamasuliridwa kuchokera kuchilankhulo cha Chigiriki ndipo Chipangano Chakale kuchokera ku Chihebri. Anagkazo ndi liwu la Chigiriki lomwe limamasuliridwa kuti “kukakamiza”.

Buy For Apple Devices
Buy From Google Books
Buy Paperback
Category:

Description

Reviews

There are no reviews yet.

Be the first to review “Anagkazo Mphamvu Yokakamiza!”

Your email address will not be published. Required fields are marked *

Title

Go to Top