Dziwani Adani Anu Osawoneka … ndi kuwagonjetsa!

Pamene muyenda mmoyo inu mukapeza kuti dziko lobisika ndi dziko lenileni ndipo dziko lakuthupi ndi chiwonetsero cha zina mwa zinthu zamu dziko lobisika. Monga mmene mulili ndi adani owoneka, inu mulinso ndi adani obisika. Kodi mungamenyane ndi mdani osamudziwa iye, ndondomeko zake, kapangidwe kake ka zinthu ndi zida zake? Bukhu ili ndi chida chofunika ku ulendo wa moyo wanu. M’bukhu ili mukaphunzira kuti adani anu obisika ndi ati, mizu yakukhala kwawo, maonekedwe awo ndi momwe mungapambanire nkhondo ndi iwo.

Bukhu labwinoli likuthandizeni kugonjetsa adani anu obisika!

Buy For Apple Devices
Buy From Google Books

Category:

Description

Reviews

There are no reviews yet.

Be the first to review “Dziwani Adani Anu Osawoneka … ndi kuwagonjetsa!”

Your email address will not be published. Required fields are marked *

Title

Go to Top