Kukhululuka Kwaphweketsedwa

“Ndipo pamene muimirira ndi kupemphera, khululukirani, ngati munthu wakulakwirani kanthu; kuti Atate wanunso ali Kumwamba akhululukire inu zolakwa zanu. Koma NGATI INU SIMUKHULULUKIRA, ATATE WANU WAKUMWAMBA SAZAKHULULUKIRA INU ZOLAKWA ZANU” (Marko 11:25-26). Kodi ndimezi zikukunjenjemeretsani? Yankho lanu lilipano.

Mu bukhu lofunikirali, muphunzira kukhululukira mosavuta – kutinso nanu musangalale ndi chikhululukiro cha Atate wanu wakumwamba. Mulole kuti bukhu ili likhale bwenzi lanu mpaka mutafika poti mukutha kukhululukira mosavuta ndi moona mtima.

Buy For Apple Devices
Buy From Google Books
Category:

Description

Reviews

There are no reviews yet.

Be the first to review “Kukhululuka Kwaphweketsedwa”

Your email address will not be published. Required fields are marked *

Title

Go to Top