Momwe Mungakhalire Mkhristu Wamphamvu

Mutalandira Yesu Khristu ngati Mbuye ndi Mpulumutsi wanu mumapulumutsidwa! Inu ndinu Mkhristu wobadwanso mwatsopano ndipo dzina lanu lalembedwa mu Bukhu la Moyo. Funso lanu ndilo: “Kodi sitepe yotsatira ndi yotani?” Pokhala Mkhristu ndi sitepe yabwino, koma ndi chiyambi chabe. Inu mukuyenera kukhala Mkhristu wabwino, wamphamvu. ‘Nanga ndichita bwanji izi?’ – M’buku ili labwino, mudzaphunzira njira zoti mutenge ndikukhala Mkhristu wamphamvu yemwe ali wokonzeka kufa kapena mkwatulo.

Buy For Apple Devices
Buy from Google books
Category:

Description

Reviews

There are no reviews yet.

Be the first to review “Momwe Mungakhalire Mkhristu Wamphamvu”

Your email address will not be published. Required fields are marked *

Title

Go to Top