Ndi Chinthu Chachikulu Kutumikira Ambuye

Mutha kukhala kuti munamvapo kuti ndi chinthu chachikulu kutumikira Ambuye; koma inu mutha kukhala kuti simunaganizire bwino momwe chili chabwino zedi kutumikira Ambuye Mulungu wathu. M’bukhu lapaderali la Dag Heward-Mills inu mukamvetsa kuti mtumiki wa Mulungu ndindani ndi momwe inu mungamutumikirire Ambuye. Mukadziwe mochita kusiyana pakati pa iwo amene amamutumikira Ambuye ndi iwo amene samutumikira Iye!
Inu mukawerengedwe ndi iwo amene amamutumikira Ambuye!

Buy For Apple Devices
Buy From Google Books
Category:

Description

Reviews

There are no reviews yet.

Be the first to review “Ndi Chinthu Chachikulu Kutumikira Ambuye”

Your email address will not be published. Required fields are marked *

Title

Go to Top