Ambuye, Ndikudziwa Mukufuna Winawake

N’chifukwa chiyani Mulungu Wamphamvuzonse angafunike munthu? Kodi Ambuye angafunike chiyani kwa iwe? Kodi ndi chiyani chimene Mulungu sangathe kuchita yekha? Kodi ndi chiyani chimene Mulungu sangathe kukwaniritsa yekha? Mulungu akufunafuna munthu amene adzayime pakati pa Iyeyo ndi munthu. Mulungu akufunafuna munthu amene adzayankhe mafunso a ana ang’onoang’ono! Mulungu akufunafuna munthu amene adzafikire ana osatetezedwa! Baibulo limanena kuti Mulungu ankafunafuna munthu…!

M’mene ukwerenga bukuli lonse, Warmth for the Heart, chikhumbo chako chokhala chombo chofunitsitsa kugwiritsidwa ntchito m’manja a Mulungu chidzaukiridwa. Sudzakhalanso wokhutira kungokhala membala wamba. Udzakhala munthu wothandiza! Udzanena ngati woimba wotchuka uja: “Ambuye, ndikudziwa kuti mukufunikira munthu! Mungandidalire ine!”

Category:

Description

Reviews

There are no reviews yet.

Be the first to review “Ambuye, Ndikudziwa Mukufuna Winawake”

Your email address will not be published. Required fields are marked *

Title

Go to Top