Gwirani Ntchito kuti Mudalitsike

Anthu ambiri amapereka maola ambiri akugwira ntchito ndi cholinga chimodzi chokha – kukhala olemera! Tsoka ilo, chuma chimawatha m’manja anthu ambiri pamene amalifuna molimbika kukhala olemera.

Chifukwa chiyani? Chifukwa amafuna kungokhala olemera, pamene pali cholinga chapamwamba, choposa chuma, chimene Mulungu amafuna kuti uzigwirira ntchito. Bukuli likufotokoza zinthu zimene Baibulo limanena kuti uyenera kupereka moyo wako kuzochita zimenezo.

M’malo mongogwira ntchito kuti ukhale wolemera, udzaphunzira kugwira ntchito chifukwa cha zinthu zapamwamba! Landirani masomphenya atsopano okhala dalitso kwa ena pamene mukuwerenga bukuli latsopano, lokopa chidwi, lolembedwa ndi Dag Heward-Mills!

Category:

Description

Reviews

There are no reviews yet.

Be the first to review “Gwirani Ntchito kuti Mudalitsike”

Your email address will not be published. Required fields are marked *

Title

Go to Top