Chilichonse chimene Mulungu amanena chimafuna kuleza mtima ndi “Mau a chipiriro changa”. Ambiri mwa malonjezano a Mulungu ndi zitsanzo za “Mau a chipiriro changa”. Mulungu amalonjeza zinthu zambiri m’Baibulo, koma ambiri mwa malonjezo amenewa amafuna chipiriro kuti akakwaniritsidwe.
Kachikenanso, Bishopu Dag Heward-Mills, akufotokoza mosamalitsa m’bukhuli, zokumana nazo za amuna aakulu a m’Baibulo amene anafunika kupirira “Mau a chipiriro changa” kuti akalandire malonjezo a Mulungu.

Reviews
There are no reviews yet.