Ku 1 Akorinto 12:28, Baibulo limatiuza za mphatso zingapo zimene Mulungu wapereka mu mpingo. Mphatso zosiyanasiyana izi pamodzi, zimathandiza mpingo wa Mulungu kuti upite patsogolo ndi mphamvu. Mphatso ya ulamuliro ndi imodzi mwa mphatso zimene Mulungu waika mu mpingo.
Kodi utsogoleri wa mpingo uyenera kuyendetsedwa bwanji? Kodi atsogoleri ampingo ayenera kuchita chiyani? Baibulo limanena momveka bwino kuti: “Mverani atsogoleri anu, nimuwagonjere: pakuti alindirira moyo wanu, monga akuwerengera;
Tiyenera kutenga mphatso ya utsogoleri mozama, ndipo bukhu lamtengo wapatali ili lolembedwa ndi Dag Heward-Mills lithandiza utsogoleri wa mpingo wanu, kayendetsedwe ka mipingo ndi ulamuliro wa mpingo munjira ya tsiku ndi tsiku!

Reviews
There are no reviews yet.