Dzipangeni Kukhala Opulumutsa Anthu

Mulungu akufuna kuti anthu onse apulumutsidwe! N’chifukwa chake anatuma Yesu Khristu kuti adzatifere. Yesu adagwiritsa ntchito magazi ake kulipira machimo athu. Ife omwe tapulumutsidwa, Mulungu akutitana kuti tikhale opulumutsa a anthu. Twapatsidwa Lamulo Lalikulu Lotumiza.

Mawu omaliza a Yesu kwa ife ndi awa: tipite kudziko lonse lapansi, tikapange ophunzira mwa anthu onse! Kodi udzayankha kuitanidwa kumeneku? Ili ndi mutu wina woyanitsa maganizo m’mndandanda wachikhalidwe wa mabuku a mauthenga a chipulumutso olembedwa ndi Dag Heward-Mills. Mosakayikira, buku ili lidzalimbikitsa wokhulupira aliyense kukwaniritsa udindo wake kwa ochimwa ndi kukhala wopulumutsa wa anthu!

Category:

Description

Reviews

There are no reviews yet.

Be the first to review “Dzipangeni Kukhala Opulumutsa Anthu”

Your email address will not be published. Required fields are marked *

Title

Go to Top