Kuzama ndi Kuchita Zambiri

Nkovuta kupangitsa munthu kumwa chakumwa ngati alibe ludzu. Ndi njala komanso ludzu la Mulugu lokha zitha kukuikani pa ulendo wozama.

Kodi mukufuna kusangalala ndi zinthu zozama za Mulungu? Ndine wotsimikiza kuti mukufuna ndicho chifukwa chake mukuwerenga bukhuli. Kumbukirani, “Odala ali akumva njala ndi ludzu la chilungamo; chifukwa adzakhuta”. Mukadzadzidwe pamene mukuzama ndi kuchita zambiri!

Category:

Description

Reviews

There are no reviews yet.

Be the first to review “Kuzama ndi Kuchita Zambiri”

Your email address will not be published. Required fields are marked *

Title

Go to Top