M’mene Mungakwaniritsire Utumiki Wanu

Palibe mwaife amene wayika dongosolo lokafika kumwamba opanda kuchita chomwe Mulungu amafuna kuti ife tikachite padziko lapansi. Ayi, olo ndi mmodzi! Ife tikufuna timalize ntchito Mulungu watipatsa ife. Bukhu ili ndilokhudza mmene mungakwanitsire utumiki wanu. Bukhu ili ndi kalondolondo ka momwe ife tingayankhire zochitika zaumulungu mmoyo mwathu – ndicholinga chosafuna kupezeka operewera patsikulo. Mukakwaniritse utumiki wanu ndipo Mulungu akanene kwa inu, “Wachita bwino, kapolo wabwino ndi okhulupirika!”

Category:

Description

Reviews

There are no reviews yet.

Be the first to review “M’mene Mungakwaniritsire Utumiki Wanu”

Your email address will not be published. Required fields are marked *

Title

Go to Top