Pali kusiyana kwakukulu pakati pa kulawa chinachake ndi kutenga nawo gawo. Kulawa chinachake ndiko kuchidya kapena kuchiyesa pa lilime; kutenga nawo gawo ndiko kupitirira kulawa ndi kuzidya. Kabukhu kakang’ono kochititsa chidwi kameneka, kolembedwa ndi Dag Heward-Mills, ndi kokamba za kutumikira Mulungu mopyola mlingo wa munthu wolawa. Mulungu akufuna kuti mutenge nawo zinthu zazikulu zimene wapereka kwa inu mu utumiki.
Palibe chifukwa chokhalira olawa pamene mungakhale otenga nawo gawo mu zinthu za Mulungu!

Reviews
There are no reviews yet.