Zomwe Zikutanthauza Kukhala M’busa

Chinthu chimodzi chokha chimadza kwa inu mukamva mawu akuti “M’busa” – nkhosa! Nkhosa ndi nyama zodalira zome zimafunikira abusa. M’busa ndi wotsogolera wosamalira komanso wachikondi kwa nkhosa. M’Baibulo, Mulungu amatitchula ife ngati gulu la nkhosa za Mulungu.
Yesu adamuuza wophunzira Petro kuti adyetse nkhosa zake kuti atsimikizire za chikondi chake cha Mpulumutsi. Kukhala m’busa ndi ntchito yabwino kwambiri. Ndi chinthu chapamwamba kuitanidwa ndi Mulungu ndi kulembetsedwa mwa antchito Ake ndi kusamalira nkhosa.
Mu bukhuli, Dag Heward-Mills akutiitanira ife, akutilimbikitsa ndi kutiwonetsa ife momwe tingatengerepo nawo mbali pa ntchito yayikulu yosamalira anthu a Mulungu. Musati muzisiyidwe kunja kwa ntchito yabwino iyi yokhala m’busa!

Category:

Description

Reviews

There are no reviews yet.

Be the first to review “Zomwe Zikutanthauza Kukhala M’busa”

Your email address will not be published. Required fields are marked *

Title

Go to Top