Baibulo ladzaza ndi mawu olimbikitsa kuti tizipemphera: “Zonse mu pemphero! Kukhala mukupemphera nthawi zonse! Anthu ayenera nthawi zonse kupemphera! Pempherani nthawi zonse! Pempherani osasiyasiya!”
M’bukuli lodabwitsali, “Zonse mu pemphero, palibe popanda pemphero”, mudzayamba ulendo wokuphunzitsani njira ndi makhalidwe a moyo wa pemphero wa Yesu Khristu. Ngati Yesu ankapemphera, ndiye kuti ine ndi iwe tiyenera kupemphera kwambiri. Chilichonse m’moyo mwathu chingakwaniritsidwe kudzera mu pemphero ndipo palibe chimene chingakwaniritsidwe popanda pemphero.
Moyo wako wa pemphero udzakhala wosangalatsa kwambiri ukatha kuwerenga bukuli losangalatsa!

Reviews
There are no reviews yet.