-
Chinthu chimodzi chokha chimadza kwa inu mukamva mawu akuti "M’busa" - nkhosa! Nkhosa ndi nyama zodalira zome zimafunikira abusa. M’busa ndi wotsogolera wosamalira komanso wachikondi kwa nkhosa. M'Baibulo, Mulungu amatitchula ife ngati gulu la nkhosa za Mulungu. Yesu adamuuza wophunzira Petro kuti adyetse nkhosa zake kuti atsimikizire za chikondi chake cha Mpulumutsi. Kukhala m'busa ndi ntchito yabwino kwambiri. Ndi chinthu chapamwamba kuitanidwa ndi Mulungu ndi kulembetsedwa mwa antchito Ake ndi kusamalira nkhosa. Mu bukhuli, Dag Heward-Mills akutiitanira ife, akutilimbikitsa ndi kutiwonetsa ife momwe tingatengerepo nawo mbali pa ntchito yayikulu yosamalira anthu a Mulungu. Musati muzisiyidwe kunja kwa ntchito yabwino iyi yokhala m’busa!
-
Kutsatira Mulungu ndi ulendo wosangalatsa wopeza zinthu. Kutsatira ndi kutengera anthu ena ndi luso lachikale lophunzirira lomwe Yesu Khristu anasankha ngati njira yaikulu yophunzitsira. M’malo mochita manyazi ndi njira yoyesedwa ndi nthawiyi, ndi nthawi yomvetsetsa kukongola ndi kudzichepetsa kwa luso la kutsatira. Mu bukhuli, muzapeza yemwe, chomwe ndi momwe mungatsatire moyenerera. Bukhu lopambana latsopanoli lolembedwa ndi Dag Heward-Mills lipereka luso la kutsatira malo ake oyenerera mu zokumana zathu za Chikhristu.
-
Kodi Chimachitika Ndi Chiyani Mukabadwa Mwatsopano? Mzimu wa Mulungu azabwera pa inu, komanso mumtima mwanu. Kenako mkati mwanu mudzabadwa kapena kupangidwanso. Mulungu amakupatsani mtima watsopano ndi mzimu zonse! Ndi mzimu wanu watsopano, mumakhala munthu watsopano kapena cholengedwa chatsopano. Mwakonzeka kukhala moyo watsopano. Moyo watsopanowu ndiwotheka chifukwa ndiwe munthu watsopano wamtima watsopano. Kubadwa mwatsopano ndikosavuta monga choncho. Anthu amafuna kuchita zinthu zovuta. Koma kubadwanso mwatsopano ndikosavuta!
-
Sokan nem vagyunk tisztában azzal, milyen módon kapcsolódik hozzánk a Bibliában található jó és a gonosz tudás fájának a története. Álláspontunk szerint azon szerencsétlen esemény kizárólag Ádámra és Évára volt hatással, nekünk már sikerült megmenekülnünk előle. Azonban ténylegesen is sikerült elmenekülnünk a jó és a gonosz tudás fájától? Ez az egyértelmű könyv segít megérteni, hogy a jó és a gonosz fája a mai napig létezik. Továbbá lerántja a leplet arról is, hogy hasonló kísértés ér minket, mint Ádámot és Évát. Mi több, olyan igazságokat oszt meg az olvasókkal, melyek segítenek átnavigáljunk az életünkön és a szolgálatunkat a könyvben található tudás segítségével. -
Mutha kukhala kuti munamvapo kuti ndi chinthu chachikulu kutumikira Ambuye; koma inu mutha kukhala kuti simunaganizire bwino momwe chili chabwino zedi kutumikira Ambuye Mulungu wathu. M'bukhu lapaderali la Dag Heward-Mills inu mukamvetsa kuti mtumiki wa Mulungu ndindani ndi momwe inu mungamutumikirire Ambuye. Mukadziwe mochita kusiyana pakati pa iwo amene amamutumikira Ambuye ndi iwo amene samutumikira Iye! Inu mukawerengedwe ndi iwo amene amamutumikira Ambuye!
-
Mu buku lopambanali, Dag Heward-Mills akusanthula zinthu zochitikadi mu utumiki masiku ano. Akukamba za zinthu zochitika zokhudza zachuma, ndale, kucheza ndi amuna kapena akazi komanso maubale mu utumiki. Bukuli ndi muuni wa makhalidwe otsatira mwambo pa mayitanidwe anu ndipo ndi buku lomwe mtsogoleri wachikhristu aliyense akuyenera kukhala nalo. Ndi lovomerezeka ku sukulu za Baibulo ndi kwa atumiki onse.
-
Anthu ambiri samamvetsetsa za malo a mtengo wa dzindikila chabwino ndi choipa m`moyo mwathu. Nthawi zambiri timaganiza kuti unali mtengo qmwe unalipo kalekale munthawi ya Adamu ndi Eva. Timakhulupirira kuti mtengo umeneyo unali ndi zipatso za poizoni zoti ukangodya yemwe wadyayo amafa. Mwa tsoka, Adamu ndi Eva anadya za mtengowu ndipo anafa. Tikawerenga za nkhaniyi, timaganiza kwa ife, “zinali zomvetsa chisoni Adam ndi Eva kudya chipatso chakuphachi koma tithokoze sitidzaikidwa m`mayeselo ndi mtengo ngati umenewo”. Zachisoni, tikhala tikulimbana ndi mtengo umenewu ndi zipatso zake. Chomwe tiyenera kudziwa ndi chakuti za mtengo wa kudzindikira chabwino ndi choipa udakalipobe mpaka lero. Umagwira ntchito m`mayesero kwa ife chimodzimodzi m`mene unapangira nthawi ya Adamu ndi Eva. Umayimilira ngati njira ina ya kwa Mulungu.
-
Keresztényként a legnagyszerűbb, legkedvesebb hatás az életedben nem lehet egyéb, mint a Szent Szellemé. Ebből a könyvből megértheted, hogyan befolyásolhatja a Szent Szellem jellemedet, lelkiismeretedet, találékonyságodat, sőt, a szentségre való képességedet is. Engedd, hogy Dag Heward-Mills fenomenális könyvén keresztül a Szent Szellem befolyásoljon, megihlessen, hasson az életedre és mindörökre megváltoztassa azt.