• Bukhu latsopanoli, "Malamulo a Ntchito ya Mpingo", ndi chida chofunikira kwambiri kwa amene ali ndi chikhumbokhumbo chogwilira ntchito mu tchalitchi. Dag Heward-Mills, mu kalembedwe kake ka nthawi zonse, akupeleka malamulo ogwilira mu utumiki wa nthawi zonse komanso kubweletsa bvumbulutso lofunikira kwambiri pa kuchita bwino mu utumiki.
  • Tonse timalindirira moyo waulemerero komwe kuzakhala "KULIBENSO THEMBERERO!" Ichi ndi chifukwa choti mmoyo timakumana ndi matsoka, kuzunzika kopitirira, utsiru, kusasangalala ndi kukhumudwa. Themberero limafotokoza bwino matsoka okumana nawowa omwe tikuwoneka kuti timakumana nawo. Tingazipewe? Pali njira yosakumanirana nazo? Bukhuli likakuthandizani inu kumvetsetsa matemberero ndi momwe mungazikhadzikitsire nokha kuti mukalandire mdalitso.
  • Szeretnél felkent lenni? Dr. Dag Heward-Mills ebben a kiemelkedő művében a kenet elnyeréséhez vezető lépéseket osztja meg az olvasóval. A könyv minden bizonnyal áldást fog jelenteni életed és szolgálatod számára. Fedezd fel, milyen lépéseket kell megtenned, hogy felkent lehess!
     
  • Mayankho ochitika ku zovuta za kayendetsedwe ka mpingo akuwonetsedweratu mu bukhu la pamwamba latsopanoli la Dag Heward-Mills
  • Bukhu limeneri ndi chotsatira chomwe chadikiridwa kwambiri cha “M’busa Wamba ndi Utumiki”. Kumaimira kusiyana kwa pakati pa utumiki wa munthu wamba ndi utumiki wa nthawi zonse. Mu bukhu lapaderali Dag Heward-Mills akukulimbikitsani kuti mukadzipereke nokha kwa thunthu kwa Mulungu ndi kukupangitsani kupeza zifukwa zoyenera zolowera mu utumiki wa nthawi zonse.
  • Keresztényként a legnagyszerűbb, legkedvesebb hatás az életedben nem lehet egyéb, mint a Szent Szellemé. Ebből a könyvből megértheted, hogyan befolyásolhatja a Szent Szellem jellemedet, lelkiismeretedet, találékonyságodat, sőt, a szentségre való képességedet is. Engedd, hogy Dag Heward-Mills fenomenális könyvén keresztül a Szent Szellem befolyásoljon, megihlessen, hasson az életedre és mindörökre megváltoztassa azt.    
     
  • Munapempherera china chake ndipo simunachipeze... Chifukwa cha kukhumudwa, munasiya kupemphera. Mwakumanapo nazo, sichoncho? Ndiye funso ndi lakuti, kodi alipo amene angapeze mayankho onse ku pemphero? Inde, inde, INDE! Pezani momwe zingathekere.
  • Anthu ambiri samamvetsetsa za malo a mtengo wa dzindikila chabwino ndi choipa m`moyo mwathu. Nthawi zambiri timaganiza kuti unali mtengo qmwe unalipo kalekale munthawi ya Adamu ndi Eva. Timakhulupirira kuti mtengo umeneyo unali ndi zipatso za poizoni zoti ukangodya yemwe wadyayo amafa. Mwa tsoka, Adamu ndi Eva anadya za mtengowu ndipo anafa. Tikawerenga za nkhaniyi, timaganiza kwa ife, “zinali zomvetsa chisoni Adam ndi Eva kudya chipatso chakuphachi koma tithokoze sitidzaikidwa m`mayeselo ndi mtengo ngati umenewo”. Zachisoni, tikhala tikulimbana ndi mtengo umenewu ndi zipatso zake. Chomwe tiyenera kudziwa ndi chakuti za mtengo wa kudzindikira chabwino ndi choipa udakalipobe mpaka lero. Umagwira ntchito m`mayesero kwa ife chimodzimodzi m`mene unapangira nthawi ya Adamu ndi Eva. Umayimilira ngati njira ina ya kwa Mulungu.
  • Mu buku lopambanali, Dag Heward-Mills akusanthula zinthu zochitikadi mu utumiki masiku ano. Akukamba za zinthu zochitika zokhudza zachuma, ndale, kucheza ndi amuna kapena akazi komanso maubale mu utumiki. Bukuli ndi muuni wa makhalidwe otsatira mwambo pa mayitanidwe anu ndipo ndi buku lomwe mtsogoleri wachikhristu aliyense akuyenera kukhala nalo. Ndi lovomerezeka ku sukulu za Baibulo ndi kwa atumiki onse.
  • Mutha kukhala kuti munamvapo kuti ndi chinthu chachikulu kutumikira Ambuye; koma inu mutha kukhala kuti simunaganizire bwino momwe chili chabwino zedi kutumikira Ambuye Mulungu wathu. M'bukhu lapaderali la Dag Heward-Mills inu mukamvetsa kuti mtumiki wa Mulungu ndindani ndi momwe inu mungamutumikirire Ambuye. Mukadziwe mochita kusiyana pakati pa iwo amene amamutumikira Ambuye ndi iwo amene samutumikira Iye! Inu mukawerengedwe ndi iwo amene amamutumikira Ambuye!
  • Sokan nem vagyunk tisztában azzal, milyen módon kapcsolódik hozzánk a Bibliában található jó és a gonosz tudás fájának a története. Álláspontunk szerint azon szerencsétlen esemény kizárólag Ádámra és Évára volt hatással, nekünk már sikerült megmenekülnünk előle. Azonban ténylegesen is sikerült elmenekülnünk a jó és a gonosz tudás fájától? Ez az egyértelmű könyv segít megérteni, hogy a jó és a gonosz fája a mai napig létezik. Továbbá lerántja a leplet arról is, hogy hasonló kísértés ér minket, mint Ádámot és Évát. Mi több, olyan igazságokat oszt meg az olvasókkal, melyek segítenek átnavigáljunk az életünkön és a szolgálatunkat a könyvben található tudás segítségével.    
     
  • Kodi Chimachitika Ndi Chiyani Mukabadwa Mwatsopano? Mzimu wa Mulungu azabwera pa inu, komanso mumtima mwanu. Kenako mkati mwanu mudzabadwa kapena kupangidwanso. Mulungu amakupatsani mtima watsopano ndi mzimu zonse! Ndi mzimu wanu watsopano, mumakhala munthu watsopano kapena cholengedwa chatsopano. Mwakonzeka kukhala moyo watsopano. Moyo watsopanowu ndiwotheka chifukwa ndiwe munthu watsopano wamtima watsopano. Kubadwa mwatsopano ndikosavuta monga choncho. Anthu amafuna kuchita zinthu zovuta. Koma kubadwanso mwatsopano ndikosavuta!

Title

Go to Top